Nyimbo ya Solomo 4:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Milomo yako imangokhalira kukha uchi wapachisa,+ iwe mkwatibwi wanga. Uchi+ ndi mkaka zili kuseri kwa lilime lako, ndipo kununkhira kwa zovala zako kuli ngati kununkhira+ kwa nkhalango ya Lebanoni. Nyimbo ya Solomo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 4:11 Nsanja ya Olonda,1/15/2015, tsa. 3011/15/2006, tsa. 19
11 Milomo yako imangokhalira kukha uchi wapachisa,+ iwe mkwatibwi wanga. Uchi+ ndi mkaka zili kuseri kwa lilime lako, ndipo kununkhira kwa zovala zako kuli ngati kununkhira+ kwa nkhalango ya Lebanoni.