-
Nyimbo ya Solomo 5:12Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
12 Maso ake ali ngati njiwa zimene zili pafupi ndi mtsinje wamadzi, zimene zikusamba mumkaka, zitakhala chakumphepete kwa madziwo.
-