Nyimbo ya Solomo 6:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 “Kodi wachikondi wako wapita kuti, iwe mkazi wokongola kwambiri kuposa akazi onse?+ Kodi wachikondi wako walowera kuti, kuti tikuthandize kum’funafuna?”
6 “Kodi wachikondi wako wapita kuti, iwe mkazi wokongola kwambiri kuposa akazi onse?+ Kodi wachikondi wako walowera kuti, kuti tikuthandize kum’funafuna?”