Nyimbo ya Solomo 6:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 “Ine ndinatsetserekera kumunda+ wa mitengo ya zipatso zokhala ngati mtedza, kuti ndikaone maluwa ake m’chigwa,*+ kuti ndikaone ngati mitengo ya mpesa yaphukira, ndiponso ngati mitengo ya makangaza yachita maluwa.+
11 “Ine ndinatsetserekera kumunda+ wa mitengo ya zipatso zokhala ngati mtedza, kuti ndikaone maluwa ake m’chigwa,*+ kuti ndikaone ngati mitengo ya mpesa yaphukira, ndiponso ngati mitengo ya makangaza yachita maluwa.+