Yesaya 4:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Amene adzatsale mu Ziyoni ndiponso amene adzatsale mu Yerusalemu adzakhala oyera kwa iye.+ Amenewa adzakhala anthu onse amene analembedwa mayina kuti akhale ndi moyo mu Yerusalemu.+ Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 4:3 Yesaya 1, ptsa. 67-69
3 Amene adzatsale mu Ziyoni ndiponso amene adzatsale mu Yerusalemu adzakhala oyera kwa iye.+ Amenewa adzakhala anthu onse amene analembedwa mayina kuti akhale ndi moyo mu Yerusalemu.+