-
Yesaya 4:5Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
5 Akadzatero, malo onse a paphiri la Ziyoni+ ndiponso malo onse a mu Yerusalemu ochitirapo misonkhano, Yehova adzawapangira mtambo ndi utsi kuti ziziwathandiza masana. Adzawapangiranso kuwala kwa moto walawilawi+ kuti kuziwathandiza usiku,+ ndipo pamwamba pa malo onse aulemererowo padzakhala chotchinga.+
-