Yesaya 6:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Pamenepo mserafi mmodzi anaulukira kwa ine. M’manja mwake munali khala lamoto+ limene analitenga paguwa lansembe ndi chopanira.+ Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 6:6 Yesaya 1, tsa. 93 Nsanja ya Olonda,4/1/1991, tsa. 2310/15/1987, ptsa. 16, 19
6 Pamenepo mserafi mmodzi anaulukira kwa ine. M’manja mwake munali khala lamoto+ limene analitenga paguwa lansembe ndi chopanira.+