Yesaya 9:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Pakuti kuipa kwayaka ngati moto,+ ndipo kudzanyeketsa zitsamba zaminga ndi udzu.+ Kuipako kudzayaka m’zitsamba zowirira za m’nkhalango,+ ndipo utsi wa mitengoyo udzakwera m’mwamba kuti tolo!+ Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 9:18 Yesaya 1, ptsa. 139-140
18 Pakuti kuipa kwayaka ngati moto,+ ndipo kudzanyeketsa zitsamba zaminga ndi udzu.+ Kuipako kudzayaka m’zitsamba zowirira za m’nkhalango,+ ndipo utsi wa mitengoyo udzakwera m’mwamba kuti tolo!+