Yesaya 9:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Manase adzadya Efuraimu ndipo Efuraimu adzadya Manase. Awiriwa adzaukira Yuda pamodzi.+ Chifukwa cha zonsezi, mkwiyo wake sunabwerere, ndipo dzanja lake lidakali lotambasula.+ Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 9:21 Yesaya 1, ptsa. 134, 139-140
21 Manase adzadya Efuraimu ndipo Efuraimu adzadya Manase. Awiriwa adzaukira Yuda pamodzi.+ Chifukwa cha zonsezi, mkwiyo wake sunabwerere, ndipo dzanja lake lidakali lotambasula.+