Yesaya 14:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 mudzanene mwambi uwu wotonza mfumu ya Babulo: “Uja ankagwiritsa ntchito anzakeyu wasiya ndithu! Wopondereza uja waleka ndithu!+ Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 14:4 Nsanja ya Olonda,9/15/2002, tsa. 30 Yesaya 1, ptsa. 182-183
4 mudzanene mwambi uwu wotonza mfumu ya Babulo: “Uja ankagwiritsa ntchito anzakeyu wasiya ndithu! Wopondereza uja waleka ndithu!+