Yesaya 14:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Onsewo akulankhula nawe kuti, ‘Kodi iwenso wafooketsedwa ngati ife?+ Kodi zoonadi wafanana ndi ife?+ Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 14:10 Yesaya 1, ptsa. 183-184
10 Onsewo akulankhula nawe kuti, ‘Kodi iwenso wafooketsedwa ngati ife?+ Kodi zoonadi wafanana ndi ife?+