Yesaya 14:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 amene anachititsa nthaka kukhala ngati chipululu, amene anagonjetsa mizinda ya padziko lapansi,+ ndiponso amene sanali kutsegulira njira akaidi ake kuti azipita kwawo?’+ Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 14:17 Yesaya 1, ptsa. 185-187
17 amene anachititsa nthaka kukhala ngati chipululu, amene anagonjetsa mizinda ya padziko lapansi,+ ndiponso amene sanali kutsegulira njira akaidi ake kuti azipita kwawo?’+