Yesaya 14:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Koma iweyo watayidwa popanda kuikidwa m’manda,+ ngati mphukira yonyansa imene ili pakati pa anthu akufa ophedwa ndi lupanga, amene akutsikira kumiyala ya m’dzenje.+ Watayidwa ngati mtembo wopondedwapondedwa.+ Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 14:19 Yesaya 1, ptsa. 185-187
19 Koma iweyo watayidwa popanda kuikidwa m’manda,+ ngati mphukira yonyansa imene ili pakati pa anthu akufa ophedwa ndi lupanga, amene akutsikira kumiyala ya m’dzenje.+ Watayidwa ngati mtembo wopondedwapondedwa.+