Yesaya 14:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Sudzakhalira nawo limodzi m’manda, chifukwa unawononga dziko lako lomwe, ndipo unapha anthu ako omwe. Mayina a ana a anthu ochita zoipa sadzatchulidwanso mpaka kalekale.+ Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 14:20 Yesaya 1, ptsa. 185-187
20 Sudzakhalira nawo limodzi m’manda, chifukwa unawononga dziko lako lomwe, ndipo unapha anthu ako omwe. Mayina a ana a anthu ochita zoipa sadzatchulidwanso mpaka kalekale.+