Yesaya 14:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 “Anthu inu, konzekerani kupha ana ake chifukwa cha zolakwa za makolo awo,+ kuti asalandenso dziko lapansi n’kulidzaza ndi mizinda.”+ Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 14:21 Yesaya 1, tsa. 187
21 “Anthu inu, konzekerani kupha ana ake chifukwa cha zolakwa za makolo awo,+ kuti asalandenso dziko lapansi n’kulidzaza ndi mizinda.”+