Yesaya 14:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 “Babulo ndidzamusandutsa malo okhala nungu* ndiponso malo a zithaphwi. Ndidzamusesa ndi tsache* la chiwonongeko,”+ watero Yehova wa makamu. Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 14:23 Yesaya 1, tsa. 188 Buku la Onse, ptsa. 27-29
23 “Babulo ndidzamusandutsa malo okhala nungu* ndiponso malo a zithaphwi. Ndidzamusesa ndi tsache* la chiwonongeko,”+ watero Yehova wa makamu.