Yesaya 14:32 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 32 Kodi munthu adzawayankha chiyani amithenga+ a mitundu ya anthu? Adzawayankha kuti, Yehova waika maziko a Ziyoni,+ ndipo anthu ake osautsika adzathawira mmenemo. Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 14:32 Yesaya 1, ptsa. 191-192
32 Kodi munthu adzawayankha chiyani amithenga+ a mitundu ya anthu? Adzawayankha kuti, Yehova waika maziko a Ziyoni,+ ndipo anthu ake osautsika adzathawira mmenemo.