Yesaya 30:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 amene akupita ku Iguputo+ osafunsira kwa ine,+ ndiponso amene akupita ku Iguputo kuti akapeze chitetezo kwa Farao ndi kukabisala mumthunzi wa Iguputo.+ Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 30:2 Yesaya 1, ptsa. 302-303
2 amene akupita ku Iguputo+ osafunsira kwa ine,+ ndiponso amene akupita ku Iguputo kuti akapeze chitetezo kwa Farao ndi kukabisala mumthunzi wa Iguputo.+