Yesaya 30:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Aliyense adzachita manyazi ndi anthu opanda phindu, osathandiza ndi osapindulitsa, omwe ndi ochititsa manyazi ndi otonzetsa.”+
5 Aliyense adzachita manyazi ndi anthu opanda phindu, osathandiza ndi osapindulitsa, omwe ndi ochititsa manyazi ndi otonzetsa.”+