-
Yesaya 30:26Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
26 Kuwala kwa mwezi wathunthu kudzakhala ngati kuwala kwa dzuwa lowala kwambiri. Kuwala kwa dzuwa lowala kwambiri kudzawonjezereka maulendo 7+ ndipo kudzakhala ngati kuwala kwa masiku 7. Zimenezi zidzachitika m’tsiku limene Yehova adzachiritse mtundu wake wovulala+ ndi kupoletsa+ chilonda choopsa cha anthu ake, amene iyeyo anawavulaza powalanga.
-