Yesaya 32:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Inu akazi amene mukukhala mosatekeseka, njenjemerani! Inu osasamala, chitani mantha! Vulani n’kukhala maliseche, ndipo muvale ziguduli m’chiuno mwanu.+ Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 32:11 Yesaya 1, ptsa. 338-339
11 Inu akazi amene mukukhala mosatekeseka, njenjemerani! Inu osasamala, chitani mantha! Vulani n’kukhala maliseche, ndipo muvale ziguduli m’chiuno mwanu.+