Yesaya 32:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Pakuti nsanja yokhalamo yasiyidwa,+ piringupiringu amene anali mumzindamo watha. Ofeli+ ndi nsanja ya mlonda zasanduka tchire. Mpaka kalekale zidzakhala malo osangalalako mbidzi, ndi odyetserako ziweto, Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 32:14 Yesaya 1, ptsa. 339-340
14 Pakuti nsanja yokhalamo yasiyidwa,+ piringupiringu amene anali mumzindamo watha. Ofeli+ ndi nsanja ya mlonda zasanduka tchire. Mpaka kalekale zidzakhala malo osangalalako mbidzi, ndi odyetserako ziweto,