Yesaya 36:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Ukudalira thandizo la Iguputo,+ bango lophwanyika loti munthu ataligwira kuti limuchirikize,+ lingamucheke m’manja. Umu ndi mmene Farao+ mfumu ya Iguputo alili kwa onse omudalira.+ Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 36:6 Yesaya 1, tsa. 386
6 Ukudalira thandizo la Iguputo,+ bango lophwanyika loti munthu ataligwira kuti limuchirikize,+ lingamucheke m’manja. Umu ndi mmene Farao+ mfumu ya Iguputo alili kwa onse omudalira.+