Yesaya 36:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Ngati inu mungandiuze kuti, ‘Tikudalira Yehova Mulungu wathu,’ kodi si iye amene Hezekiya wamuchotsera malo ake okwezeka+ ndi maguwa ake ansembe,+ n’kuuza Yuda ndi Yerusalemu kuti, ‘Muzigwada pamaso pa guwa lansembe ili’?”’+ Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 36:7 Yesaya 1, tsa. 386
7 Ngati inu mungandiuze kuti, ‘Tikudalira Yehova Mulungu wathu,’ kodi si iye amene Hezekiya wamuchotsera malo ake okwezeka+ ndi maguwa ake ansembe,+ n’kuuza Yuda ndi Yerusalemu kuti, ‘Muzigwada pamaso pa guwa lansembe ili’?”’+