Yesaya 36:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Pamenepo Eliyakimu,+ Sebina,+ ndi Yowa+ anauza Rabisake+ kuti: “Chonde lankhulani ndi ife atumiki anu m’chilankhulo cha Asiriya+ chifukwa timachimva. Musalankhule nafe m’chilankhulo cha Ayuda,+ kuti anthu amene ali pamakomawa asamve.”+ Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 36:11 Yesaya 1, tsa. 387
11 Pamenepo Eliyakimu,+ Sebina,+ ndi Yowa+ anauza Rabisake+ kuti: “Chonde lankhulani ndi ife atumiki anu m’chilankhulo cha Asiriya+ chifukwa timachimva. Musalankhule nafe m’chilankhulo cha Ayuda,+ kuti anthu amene ali pamakomawa asamve.”+