Yesaya 36:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Koma Eliyakimu+ mwana wa Hilikiya amene anali woyang’anira banja lachifumu,+ Sebina+ mlembi, ndi Yowa+ mwana wa Asafu wolemba zochitika, anapita kwa Hezekiya atang’amba zovala zawo+ n’kumuuza mawu a Rabisake.+
22 Koma Eliyakimu+ mwana wa Hilikiya amene anali woyang’anira banja lachifumu,+ Sebina+ mlembi, ndi Yowa+ mwana wa Asafu wolemba zochitika, anapita kwa Hezekiya atang’amba zovala zawo+ n’kumuuza mawu a Rabisake.+