Yesaya 40:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Iwo sanabzalidwe n’komwe ndipo sanafesedwe. Chitsa chawo sichinazike mizu munthaka.+ Munthu akhoza kungowauzira iwo n’kuuma,+ ndipo mphepo yamkuntho idzawauluza ngati mapesi.+
24 Iwo sanabzalidwe n’komwe ndipo sanafesedwe. Chitsa chawo sichinazike mizu munthaka.+ Munthu akhoza kungowauzira iwo n’kuuma,+ ndipo mphepo yamkuntho idzawauluza ngati mapesi.+