Yesaya 43:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Pakuti ine ndine Yehova Mulungu wako, Woyera wa Isiraeli ndiponso Mpulumutsi wako.+ Ndapereka Iguputo monga dipo* lokuwombolera.+ Ndaperekanso Itiyopiya+ ndi Seba m’malo mwako. Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 43:3 Yesaya 2, ptsa. 48-49
3 Pakuti ine ndine Yehova Mulungu wako, Woyera wa Isiraeli ndiponso Mpulumutsi wako.+ Ndapereka Iguputo monga dipo* lokuwombolera.+ Ndaperekanso Itiyopiya+ ndi Seba m’malo mwako.