Yesaya 43:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 “Bweretsa anthu akhungu ngakhale kuti ali ndi maso, ndiponso anthu ogontha ngakhale kuti ali ndi makutu.+ Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 43:8 Yesaya 2, ptsa. 46-47
8 “Bweretsa anthu akhungu ngakhale kuti ali ndi maso, ndiponso anthu ogontha ngakhale kuti ali ndi makutu.+