Yesaya 45:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Yehova, Woyera wa Isiraeli+ ndiponso amene anamuumba,+ wanena kuti: “Ndifunseni za zinthu zimene zikubwera+ zokhudza ana anga.+ Ndipo pa zinthu zokhudza ntchito+ ya manja anga mundifunse kuti ndikuyankheni. Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 45:11 Yesaya 2, ptsa. 85-86
11 Yehova, Woyera wa Isiraeli+ ndiponso amene anamuumba,+ wanena kuti: “Ndifunseni za zinthu zimene zikubwera+ zokhudza ana anga.+ Ndipo pa zinthu zokhudza ntchito+ ya manja anga mundifunse kuti ndikuyankheni.