Yesaya 45:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Ndalumbira pa ine mwini.+ Mawuwo atuluka m’kamwa mwanga m’chilungamo,+ moti sadzabwerera.+ Ndalumbira kuti bondo lililonse lidzagwadira ine+ ndipo lilime lililonse lidzalumbira kwa ine,+ Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 45:23 Yesaya 2, ptsa. 91-92
23 Ndalumbira pa ine mwini.+ Mawuwo atuluka m’kamwa mwanga m’chilungamo,+ moti sadzabwerera.+ Ndalumbira kuti bondo lililonse lidzagwadira ine+ ndipo lilime lililonse lidzalumbira kwa ine,+