Yesaya 48:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Zinthu zimene ndikulengazi n’zatsopano, si zinthu zakale ayi. Ndi zinthu zimene simunazimvepo m’mbuyomu. Ndikuchita izi chifukwa munganene kuti, ‘Ifetu tinali kuzidziwa kale zimenezi.’+ Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 48:7 Yesaya 2, ptsa. 123-125
7 Zinthu zimene ndikulengazi n’zatsopano, si zinthu zakale ayi. Ndi zinthu zimene simunazimvepo m’mbuyomu. Ndikuchita izi chifukwa munganene kuti, ‘Ifetu tinali kuzidziwa kale zimenezi.’+