Yesaya 48:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Ndithu, ndidzachitapo kanthu chifukwa cha dzina langa.+ Pakuti munthu angalekerere bwanji dzina lake likuipitsidwa?+ Ulemerero wanga sindidzaupereka kwa wina aliyense.+ Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 48:11 Yesaya 2, ptsa. 126-127
11 Ndithu, ndidzachitapo kanthu chifukwa cha dzina langa.+ Pakuti munthu angalekerere bwanji dzina lake likuipitsidwa?+ Ulemerero wanga sindidzaupereka kwa wina aliyense.+