Yesaya 48:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 “Sonkhanani pamodzi anthu nonsenu kuti mumve.+ Ndani pakati pawo ananenapo zinthu zimenezi? Iye amene Yehova wamukonda+ adzachitira Babulo zimene akufuna.+ Dzanja lake lidzakhala pa Akasidi.+ Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 48:14 Yesaya 2, tsa. 130
14 “Sonkhanani pamodzi anthu nonsenu kuti mumve.+ Ndani pakati pawo ananenapo zinthu zimenezi? Iye amene Yehova wamukonda+ adzachitira Babulo zimene akufuna.+ Dzanja lake lidzakhala pa Akasidi.+