Yesaya 48:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Ineyo ndalankhula, komanso ndamuitana.+ Ndamubweretsa, ndipo ndidzachititsa kuti zochita zake zimuyendere bwino.+ Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 48:15 Yesaya 2, tsa. 130
15 Ineyo ndalankhula, komanso ndamuitana.+ Ndamubweretsa, ndipo ndidzachititsa kuti zochita zake zimuyendere bwino.+