Yesaya 48:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Mbadwa zanu zochokera mkati mwa matupi anu zidzakhala ngati mchenga.+ Dzina lawo silidzatha kapena kuwonongedwa pamaso panga.”+ Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 48:19 Yesaya 2, tsa. 132
19 Mbadwa zanu zochokera mkati mwa matupi anu zidzakhala ngati mchenga.+ Dzina lawo silidzatha kapena kuwonongedwa pamaso panga.”+