Yesaya 54:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 “Pakuti Wokupanga Wamkulu+ ndiye mwamuna wako.+ Dzina lake ndi Yehova wa makamu,+ ndipo Woyera wa Isiraeli ndiye Wokuwombola.+ Iye adzatchedwa Mulungu wa dziko lonse lapansi.+ Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 54:5 Nsanja ya Olonda,1/1/1986, tsa. 30
5 “Pakuti Wokupanga Wamkulu+ ndiye mwamuna wako.+ Dzina lake ndi Yehova wa makamu,+ ndipo Woyera wa Isiraeli ndiye Wokuwombola.+ Iye adzatchedwa Mulungu wa dziko lonse lapansi.+