Yesaya 55:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 M’malo mwa chitsamba chaminga padzamera mtengo wa mkungudza.+ M’malo mwa chomera choyabwa padzamera mtengo wa mchisu.+ Zimenezi zidzamutchukitsa Yehova,+ ndipo zidzakhala chizindikiro choti sichidzachotsedwa mpaka kalekale.”+ Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 55:13 Yesaya 2, ptsa. 245-246
13 M’malo mwa chitsamba chaminga padzamera mtengo wa mkungudza.+ M’malo mwa chomera choyabwa padzamera mtengo wa mchisu.+ Zimenezi zidzamutchukitsa Yehova,+ ndipo zidzakhala chizindikiro choti sichidzachotsedwa mpaka kalekale.”+