Yesaya 56:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Alonda ake ndi akhungu+ ndipo sakudziwa chilichonse.+ Onsewo ndi agalu opanda mawu. Satha kuuwa.+ Amangokhalira kupuma wefuwefu ndi kugona pansi. Amakonda kugona tulo.+ Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 56:10 Yesaya 2, ptsa. 258-260
10 Alonda ake ndi akhungu+ ndipo sakudziwa chilichonse.+ Onsewo ndi agalu opanda mawu. Satha kuuwa.+ Amangokhalira kupuma wefuwefu ndi kugona pansi. Amakonda kugona tulo.+