Yesaya 56:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Iwo ndi agalu adyera kwambiri+ ndipo sakhuta,+ komanso ndi abusa osamvetsa zinthu.+ Aliyense wa iwo wapatukira kunjira yake n’cholinga chopeza phindu lachinyengo lochokera m’dera lake.+ Iwo amati: Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 56:11 Yesaya 2, ptsa. 258-260
11 Iwo ndi agalu adyera kwambiri+ ndipo sakhuta,+ komanso ndi abusa osamvetsa zinthu.+ Aliyense wa iwo wapatukira kunjira yake n’cholinga chopeza phindu lachinyengo lochokera m’dera lake.+ Iwo amati: