Yesaya 57:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 “Koma anthu inu bwerani pafupi,+ inu ana a mayi wolosera zam’tsogolo,+ mbewu ya munthu wachigololo ndi ya mkazi wochita uhule:+ Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 57:3 Yesaya 2, ptsa. 263-264
3 “Koma anthu inu bwerani pafupi,+ inu ana a mayi wolosera zam’tsogolo,+ mbewu ya munthu wachigololo ndi ya mkazi wochita uhule:+