Yesaya 57:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Bedi lako unaliika pamwamba pa phiri lalitali ndi lokwezeka.+ Unapitanso kumeneko kukapereka nsembe.+ Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 57:7 Yesaya 2, tsa. 265
7 Bedi lako unaliika pamwamba pa phiri lalitali ndi lokwezeka.+ Unapitanso kumeneko kukapereka nsembe.+