8 Unaika chizindikiro chachikumbutso chako kuseri kwa chitseko ndi kuseri kwa felemu.+ Iwe unavula n’kukwera mtunda kupita kumeneko uli kutali ndi ine. Unakulitsa bedi lako,+ ndipo unachita nawo pangano. Unkakonda kugona nawo pabedi+ ndipo unaona chiwalo cha mwamuna.