Yesaya 57:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Wakhala ukugwira ntchito mwamphamvu m’njira zako zambirimbiri.+ Sunanene kuti, ‘N’zopanda phindu!’ Wapezanso mphamvu zina.+ N’chifukwa chake sunadwale.+ Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 57:10 Yesaya 2, tsa. 268
10 Wakhala ukugwira ntchito mwamphamvu m’njira zako zambirimbiri.+ Sunanene kuti, ‘N’zopanda phindu!’ Wapezanso mphamvu zina.+ N’chifukwa chake sunadwale.+