Yesaya 57:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 “Kodi unachita mantha ndi ndani kuti uyambe kuopa,+ mpaka kuyamba kunama?+ Koma sunakumbukire ine.+ Palibe chimene unaganizira mumtima mwako.+ Popeza ine ndinakhala chete ndipo sindinachitepo kanthu pa zochita zako,+ iweyo sunali kundiopa.+ Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 57:11 Yesaya 2, tsa. 269
11 “Kodi unachita mantha ndi ndani kuti uyambe kuopa,+ mpaka kuyamba kunama?+ Koma sunakumbukire ine.+ Palibe chimene unaganizira mumtima mwako.+ Popeza ine ndinakhala chete ndipo sindinachitepo kanthu pa zochita zako,+ iweyo sunali kundiopa.+