Yesaya 57:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Pakuti ine sindidzatsutsana nanu mpaka kalekale, ndiponso sindidzakhala wokwiya mpaka kalekale.+ Popeza chifukwa cha ine, mzimu wa munthu ukhoza kufooka,+ ngakhalenso zinthu zopuma zimene ineyo ndinapanga.+ Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 57:16 Yesaya 2, tsa. 271
16 Pakuti ine sindidzatsutsana nanu mpaka kalekale, ndiponso sindidzakhala wokwiya mpaka kalekale.+ Popeza chifukwa cha ine, mzimu wa munthu ukhoza kufooka,+ ngakhalenso zinthu zopuma zimene ineyo ndinapanga.+