Yesaya 60:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Pa nthawi imeneyo, nkhope yako idzasangalala ukadzaona zimenezi.+ Mtima wako udzanthunthumira ndi kufutukuka, chifukwa chuma cha m’nyanja chidzabwera kwa iwe. Katundu wa mitundu ya anthu adzabwera kwa iwe.+ Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 60:5 Nsanja ya Olonda,7/1/2002, tsa. 11 Yesaya 2, ptsa. 307-308, 310
5 Pa nthawi imeneyo, nkhope yako idzasangalala ukadzaona zimenezi.+ Mtima wako udzanthunthumira ndi kufutukuka, chifukwa chuma cha m’nyanja chidzabwera kwa iwe. Katundu wa mitundu ya anthu adzabwera kwa iwe.+