Yesaya 60:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Chikhamu cha ngamila zamphongo zing’onozing’ono za ku Midiyani ndi ku Efa+ chidzadzaza dziko lako. Anthu onse a ku Sheba+ adzabwera atanyamula golide ndi lubani. Iwo adzatamanda Yehova pamaso pa anthu onse.+ Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 60:6 Nsanja ya Olonda,7/1/2002, tsa. 11 Yesaya 2, tsa. 308
6 Chikhamu cha ngamila zamphongo zing’onozing’ono za ku Midiyani ndi ku Efa+ chidzadzaza dziko lako. Anthu onse a ku Sheba+ adzabwera atanyamula golide ndi lubani. Iwo adzatamanda Yehova pamaso pa anthu onse.+