Yesaya 60:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 “Zipata zako zidzakhala zotsegula nthawi zonse.+ Sizidzatsekedwa usana ndi usiku kuti chuma cha mitundu ya anthu chibwere kwa iwe,+ ndipo mafumu awo ndiwo adzakhale patsogolo pochita zimenezi.+ Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 60:11 Nsanja ya Olonda,7/1/2002, ptsa. 13-141/1/2000, tsa. 13 Yesaya 2, ptsa. 311-314
11 “Zipata zako zidzakhala zotsegula nthawi zonse.+ Sizidzatsekedwa usana ndi usiku kuti chuma cha mitundu ya anthu chibwere kwa iwe,+ ndipo mafumu awo ndiwo adzakhale patsogolo pochita zimenezi.+