Yesaya 60:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 “Ana a anthu okusautsa adzabwera kwa iwe atawerama.+ Onse amene anali kukuchitira chipongwe adzagwada pamapazi ako,+ ndipo adzakutcha mzinda wa Yehova, Ziyoni+ wa Woyera wa Isiraeli. Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 60:14 Yesaya 2, tsa. 315 Nsanja ya Olonda,1/1/2000, tsa. 14
14 “Ana a anthu okusautsa adzabwera kwa iwe atawerama.+ Onse amene anali kukuchitira chipongwe adzagwada pamapazi ako,+ ndipo adzakutcha mzinda wa Yehova, Ziyoni+ wa Woyera wa Isiraeli.